Hoseya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Efuraimu ataona matenda ake ndiponso Yuda ataona chilonda chake,Efuraimu anapita ku Asuri+ komanso anatumiza anthu kwa mfumu yaikulu. Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani.Ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.
13 Efuraimu ataona matenda ake ndiponso Yuda ataona chilonda chake,Efuraimu anapita ku Asuri+ komanso anatumiza anthu kwa mfumu yaikulu. Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani.Ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.