Zefaniya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova Mulungu wako ali pakati panu+ Ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu. Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, Ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.
17 Yehova Mulungu wako ali pakati panu+ Ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu. Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, Ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.