Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+ Salimo 147:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yakobo amamuuza mawu ake,Ndipo Isiraeli amamuuza malangizo ake komanso zigamulo zake.+ 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake. Tamandani Ya!*+
5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
6 Chifukwa ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+
19 Yakobo amamuuza mawu ake,Ndipo Isiraeli amamuuza malangizo ake komanso zigamulo zake.+ 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake. Tamandani Ya!*+