Amosi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Yehova adzabangula ku Ziyoni,Ndipo adzafuula ku Yerusalemu. Malo amene abusa amadyetserako ziweto adzalira,Ndipo pansonga ya phiri la Karimeli padzauma.”+
2 Iye anati: “Yehova adzabangula ku Ziyoni,Ndipo adzafuula ku Yerusalemu. Malo amene abusa amadyetserako ziweto adzalira,Ndipo pansonga ya phiri la Karimeli padzauma.”+