Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Choncho ndinanena kuti: “Sindidzanenanso za iye,

      Ndipo sindidzalankhulanso mʼdzina lake.”+

      Koma mumtima mwangamu, mawu ake anali ngati moto woyaka umene watsekeredwa mʼmafupa anga,

      Ndipo ndinatopa ndi kudziletsa kuti ndisalankhule

      Moti sindikanathanso kupirira.+

  • Amosi 7:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Amosi anayankha Amaziya kuti: “Ine sindinali mneneri kapena mwana wa mneneri, koma ndinali mʼbusa+ ndiponso wosamalira* nkhuyu. 15 Koma Yehova ananditenga kumene ndinkaweta nkhosa ndipo Yehova anandiuza kuti, ‘Pita ukanenere kwa anthu anga Aisiraeli.’+

  • Machitidwe 4:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma Petulo ndi Yohane anawayankha kuti: “Weruzani nokha, ngati nʼzoyenera pamaso pa Mulungu kumvera inu mʼmalo momvera Mulunguyo. 20 Koma ife sitingasiye kulankhula za zinthu zimene tinaziona ndi kuzimva.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena