Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Lupanga lidzazungulira mʼmizinda yake+

      Ndipo lidzawononga mipiringidzo nʼkupha anthu chifukwa cha zoipa zimene ankafuna kuchita.+

  • Amosi 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndalumbira pa dzina langaʼ+ kuti,

      ‘Ndimanyasidwa ndi kunyada kwa Yakobo,+

      Ndimadana ndi nsanja zake zolimba,+

      Ndipo ndidzapereka mzindawu ndi zinthu zake zonse kwa adani ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena