Salimo 130:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 130 Inu Yehova, pa nthawi imene zinthu zinandivuta kwambiri ndinaitana pa inu.+ 2 Inu Yehova, imvani mawu anga. Makutu anu amve kuchonderera kwanga kopempha thandizo.
130 Inu Yehova, pa nthawi imene zinthu zinandivuta kwambiri ndinaitana pa inu.+ 2 Inu Yehova, imvani mawu anga. Makutu anu amve kuchonderera kwanga kopempha thandizo.