Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 28:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova adzaimirira ngati mmene anachitira paphiri la Perazimu.

      Adzaimirira ngati mmene anachitira mʼchigwa, pafupi ndi Gibiyoni,+

      Kuti achite zochita zake, zochita zake zodabwitsa,

      Komanso kuti agwire ntchito yake, ntchito yake yachilendo.+

  • Yesaya 29:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho, ine ndi amene ndidzachitenso zinthu zodabwitsa ndi anthu awa,+

      Ndidzachita zodabwitsa mʼnjira yodabwitsa.

      Nzeru za anthu awo anzeru zidzatha,

      Ndipo kumvetsetsa zinthu kwa anthu awo ozindikira kudzabisika.”+

  • Maliro 4:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova wasonyeza ukali wake.

      Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+

      Ndipo iye wayatsa moto mʼZiyoni, umene wawotcha maziko ake.+

      ל [Lamed]

      12 Mafumu apadziko lapansi ndiponso anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi,

      Sanayembekezere kuti mdani angadzalowe pamageti a Yerusalemu.+

  • Machitidwe 13:40, 41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Choncho samalani kuti zimene aneneri analemba zisakugwereni, zomwe zimati: 41 ‘Inu onyoza onani zimene ine ndikuchita nʼkudabwa nazo. Kenako mudzatha, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pangʼono zimene ndidzachite mʼmasiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena