-
Yeremiya 22:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Iwo adzadula mitengo yako ya mkungudza yabwino kwambiri
Ndipo adzaigwetsera pamoto.+
-
-
Yeremiya 46:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo+ wonena za gulu la asilikali a Farao Neko,+ mfumu ya Iguputo, amene anagonjetsedwa ndi Nebukadinezara* mfumu ya Babulo ku Karikemisi, mʼmbali mwa mtsinje wa Firate. Anagonjetsedwa ndi mfumu imeneyi mʼchaka cha 4 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Uthengawo unali wakuti:
-