-
Salimo 114:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
114 Isiraeli atatuluka mu Iguputo,+
Nyumba ya Yakobo itatuluka pakati pa anthu olankhula chilankhulo chachilendo,
-
Nahumu 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Dziko lapansi lidzanjenjemera chifukwa cha nkhope yake
Pamodzi ndi nthaka komanso zinthu zonse zokhala mʼdzikomo.+
-
-
-