Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Taonani! Mdani adzabwera ngati mitambo yamvula,

      Ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho.+

      Mahatchi ake ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga.+

      Tsoka latigwera chifukwa tawonongedwa.

  • Maliro 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Anthu amene ankatithamangitsa anali aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka mʼmwamba.+

      Iwo anatithamangitsa mʼmapiri. Anatibisalira mʼchipululu.

  • Ezekieli 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ku Lebanoni+ kunabwera chiwombankhanga chachikulu+ cha mapiko akuluakulu komanso ataliatali. Chiwombankhangacho chinali ndi nthenga zambiri zamitundu yosiyanasiyana. Chitafika kumeneko, chinathyola nsonga ya mtengo wa mkungudza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena