17 Ana amene Yekoniya anabereka ali mkaidi anali Salatiyeli, 18 Malikiramu, Pedaya, Senazara, Yekamiya, Hosama ndi Nedabiya. 19 Ana a Pedaya anali Zerubabele+ ndi Simeyi. Ana a Zerubabele anali Mesulamu ndi Hananiya (Selomiti anali mchemwali wawo).
9 “Manja a Zerubabele anayala maziko a nyumbayi+ ndipo manja ake omwewo adzaimalizitsa.+ Ndipo mudzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa inu.