Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’ Zekariya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Popeza munali temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a mʼnyumba ya Yuda ndi a mʼnyumba ya Isiraeli ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Limbani mtima,+ musachite mantha.’+
10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’
13 Popeza munali temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a mʼnyumba ya Yuda ndi a mʼnyumba ya Isiraeli ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Limbani mtima,+ musachite mantha.’+