Oweruza 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amuna 300 aja anapitiriza kuliza malipenga, ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Asilikaliwo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.
22 Amuna 300 aja anapitiriza kuliza malipenga, ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Asilikaliwo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.