Yeremiya 49:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Mpanda wa Damasiko ndidzauyatsa moto,Ndipo motowo udzawotcha nsanja zokhala ndi mipanda yolimba za Beni-hadadi.”+ Amosi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+
27 “Mpanda wa Damasiko ndidzauyatsa moto,Ndipo motowo udzawotcha nsanja zokhala ndi mipanda yolimba za Beni-hadadi.”+
3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+