-
Ezekieli 27:32, 33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Polira adzaimba nyimbo yoimba polira ndipo adzakuimbira kuti:
‘Ndi ndani angafanane ndi Turo, amene wawonongedwa* pakati pa nyanja?+
33 Katundu wako atabwera kuchokera pakatikati pa nyanja, unasangalatsa anthu ambiri.+
Chuma chako chochuluka komanso malonda ako zinalemeretsa mafumu apadziko lapansi.+
-