Ekisodo 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dziko limene ndidzakupatsani lidzayambira ku Nyanja Yofiira mpaka kunyanja ya Afilisiti, ndiponso kuyambira kuchipululu mpaka ku Mtsinje.*+ Ndidzachita zimenezi chifukwa anthu okhala mʼdzikomo ndidzawapereka mʼmanja mwanu ndipo inu mudzawathamangitsa pamaso panu.+ Salimo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tandipempha, ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kuti ikhale cholowa chako,Ndiponso dziko lonse lapansi kuti likhale lako.+ Salimo 72:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+
31 Dziko limene ndidzakupatsani lidzayambira ku Nyanja Yofiira mpaka kunyanja ya Afilisiti, ndiponso kuyambira kuchipululu mpaka ku Mtsinje.*+ Ndidzachita zimenezi chifukwa anthu okhala mʼdzikomo ndidzawapereka mʼmanja mwanu ndipo inu mudzawathamangitsa pamaso panu.+
8 Tandipempha, ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kuti ikhale cholowa chako,Ndiponso dziko lonse lapansi kuti likhale lako.+
8 Iye adzakhala ndi anthu omugonjera* kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,Komanso kuchokera ku Mtsinje* kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+