Yesaya 49:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuti ndiuze akaidi kuti, ‘Tulukani!’+ Ndiponso amene ali mumdima+ kuti, ‘Bwerani poyera kuti anthu akuoneni!’ Iwo adzadya msipu mʼmphepete mwa msewu,Ndipo mʼmphepete mwa njira zonse zimene zimadutsidwadutsidwa* mudzakhala malo awo odyeramo msipu.
9 Kuti ndiuze akaidi kuti, ‘Tulukani!’+ Ndiponso amene ali mumdima+ kuti, ‘Bwerani poyera kuti anthu akuoneni!’ Iwo adzadya msipu mʼmphepete mwa msewu,Ndipo mʼmphepete mwa njira zonse zimene zimadutsidwadutsidwa* mudzakhala malo awo odyeramo msipu.