-
Yesaya 62:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Udzakhala chisoti chokongola mʼdzanja la Yehova,
Ndiponso nduwira yachifumu mʼdzanja la Mulungu wako.
-
-
Zefaniya 3:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pa nthawiyo ndidzakubweretsani,
Ndidzachita zimenezi pa nthawi imene ndidzakusonkhanitseni.
-