Yesaya 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova walumbira atakweza dzanja lake lamanja ndiponso mkono wake wamphamvu kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu kuti chikhale chakudya chawo,Ndipo alendo sadzamwa vinyo wanu watsopano amene munamupeza movutikira.+ Yoweli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi imeneyo mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera.+Mʼmapiri angʼonoangʼono mudzayenda mkaka.Ndipo mʼmitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe adzatuluka mʼnyumba ya Yehova,+Ndipo adzathirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe. Amosi 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika,Pamene wolima adzapitirira wokolola,Ndipo woponda mphesa adzapitirira wonyamula mbewu.+Mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera+Ndipo mʼmapiri angʼonoangʼono muzidzatuluka vinyo wambiri.+
8 Yehova walumbira atakweza dzanja lake lamanja ndiponso mkono wake wamphamvu kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu kuti chikhale chakudya chawo,Ndipo alendo sadzamwa vinyo wanu watsopano amene munamupeza movutikira.+
18 Nthawi imeneyo mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera.+Mʼmapiri angʼonoangʼono mudzayenda mkaka.Ndipo mʼmitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe adzatuluka mʼnyumba ya Yehova,+Ndipo adzathirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.
13 Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika,Pamene wolima adzapitirira wokolola,Ndipo woponda mphesa adzapitirira wonyamula mbewu.+Mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera+Ndipo mʼmapiri angʼonoangʼono muzidzatuluka vinyo wambiri.+