-
Zekariya 11:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ine ndinayamba kuweta nkhosa zimene zinayenera kuphedwa+ ndipo ndinachita zimenezi chifukwa cha inu, anthu ovutika a mʼgulu la nkhosali. Choncho ndinatenga ndodo ziwiri. Ina ndinaipatsa dzina lakuti Wosangalatsa ndipo inayo ndinaipatsa dzina lakuti Mgwirizano.+ Ndiyeno ndinayamba kuweta gulu la nkhosalo.
-