Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wadzudzula abusa amene akuweta anthu ake kuti: “Inu mwabalalitsa nkhosa zanga. Munapitiriza kuzimwaza ndipo simunazisamalire.”+

      “Tsopano ndikulangani chifukwa cha zochita zanu zoipa,” akutero Yehova.

  • Ezekieli 34:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nkhosa zanga zinasochera mʼmapiri onse ndi mʼzitunda zonse zitalizitali. Nkhosa zanga zinabalalika padziko lonse lapansi ndipo panalibe amene ankazifufuza kapena kuziyangʼanayangʼana.

  • Mateyu 9:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ataona chigulu cha anthu, iye anawamvera chisoni,+ chifukwa anali onyukanyuka komanso opanda wowasamalira ngati nkhosa zimene zilibe mʼbusa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena