Ezekieli 36:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera.+ Ndidzakuyeretsani pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+ Ezekieli 36:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 ‘Ndidzakupulumutsani ku zinthu zanu zonse zodetsa ndipo ndidzauza mbewu kuti zibereke kwambiri moti sindidzakubweretseraninso njala.+
25 Ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera.+ Ndidzakuyeretsani pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+
29 ‘Ndidzakupulumutsani ku zinthu zanu zonse zodetsa ndipo ndidzauza mbewu kuti zibereke kwambiri moti sindidzakubweretseraninso njala.+