Ekisodo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wanu molakwika,+ chifukwa Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina Lake molakwika osamulanga.+
7 Musagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wanu molakwika,+ chifukwa Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina Lake molakwika osamulanga.+