Miyambo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Amene amabera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+Koma amene amakomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+
31 Amene amabera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+Koma amene amakomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+
4 Tamverani! Malipiro amene simunapereke kwa anthu amene anagwira ntchito yokolola mʼminda yanu akufuula ndipo Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba wamva kufuula kopempha thandizo kwa anthu okololawo.+