Ekisodo 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamapondereze mlendo amene akukhala nanu. Inu mukudziwa mmene zimakhalira ukakhala mlendo, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+ Zekariya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye, mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosauka.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+
9 Musamapondereze mlendo amene akukhala nanu. Inu mukudziwa mmene zimakhalira ukakhala mlendo, chifukwa inunso munali alendo mʼdziko la Iguputo.+
10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye, mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosauka.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+