Levitiko 27:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chakhumi chilichonse+ cha zinthu zamʼdzikolo, kaya ndi zokolola zamʼmunda kapena zipatso zamʼmitengo, ndi za Yehova. Chakhumi chimenechi ndi chopatulika kwa Yehova. Deuteronomo 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumapeto kwa zaka zitatu zilizonse muzidzabweretsa chakhumi cha zokolola zanu zonse mʼchaka chachitatucho, ndipo muzidzachisiya mkati mwa mzinda wanu.+
30 Chakhumi chilichonse+ cha zinthu zamʼdzikolo, kaya ndi zokolola zamʼmunda kapena zipatso zamʼmitengo, ndi za Yehova. Chakhumi chimenechi ndi chopatulika kwa Yehova.
28 Kumapeto kwa zaka zitatu zilizonse muzidzabweretsa chakhumi cha zokolola zanu zonse mʼchaka chachitatucho, ndipo muzidzachisiya mkati mwa mzinda wanu.+