Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamene mukudya chakudya cha chaka chapita, mudzafunika kuchitulutsa kuti mupeze malo oikapo chatsopano.

  • 2 Mbiri 31:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Azariya, wansembe wamkulu wa nyumba ya Zadoki, anamuyankha kuti: “Kuyambira pamene anthu anayamba kubweretsa zopereka mʼnyumba ya Yehova,+ anthu akhala akudya mpaka kukhuta ndipo pali zotsala zambiri, chifukwa Yehova wadalitsa anthu ake moti zonse mukuzionazi nʼzotsala.”+

  • Miyambo 3:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+

      Ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.*+

      10 Ukatero nyumba zako zosungiramo zinthu zidzadzaza kwambiri,+

      Ndipo zoponderamo mphesa zako zidzasefukira ndi vinyo watsopano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena