Salimo 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mukudziwa bwino za kuthawathawa kwanga.+ Sungani misozi yanga mʼthumba lanu lachikopa.+ Kodi misozi yanga sinalembedwe mʼbuku lanu?+ Salimo 69:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mayina awo afufutidwe mʼbuku la anthu amoyo,*+Ndipo iwo asalembedwe mʼbuku limene muli mayina a anthu olungama.+ Yesaya 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, pamene tikutsatira njira ya ziweruzo zanu,Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tikulakalaka dzina lanu komanso zimene dzinalo limaimira.*
8 Inu mukudziwa bwino za kuthawathawa kwanga.+ Sungani misozi yanga mʼthumba lanu lachikopa.+ Kodi misozi yanga sinalembedwe mʼbuku lanu?+
28 Mayina awo afufutidwe mʼbuku la anthu amoyo,*+Ndipo iwo asalembedwe mʼbuku limene muli mayina a anthu olungama.+
8 Inu Yehova, pamene tikutsatira njira ya ziweruzo zanu,Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tikulakalaka dzina lanu komanso zimene dzinalo limaimira.*