Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi. Nthawi yokolola ikuimira mapeto a nthawi* ino ndipo okololawo ndi angelo.

  • Mateyu 13:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ndi mmenenso zidzakhalire pamapeto a nthawi* ino. Angelo adzapita nʼkukachotsa oipa pakati pa olungama

  • Mateyu 24:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, ophunzira anabwera kwa iye ali payekha nʼkumufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino+ chidzakhala chiyani?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena