-
Maliko 6:55Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
55 Choncho anthu anathamanga uku ndi uku mʼdera lonselo nʼkuyamba kunyamula pamachira anthu onse amene ankadwala, kupita nawo kumene anamva kuti iye ali kumeneko.
-