-
Machitidwe 5:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiponso anthu ambiri ochokera mʼmizinda yozungulira Yerusalemu ankapita kumeneko ndi anthu odwala komanso amene mizimu yoipa inkawazunza. Ndipo onsewo ankachiritsidwa.
-