Mateyu 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa akudwala matenda akugwa ndipo akuvutika kwambiri. Nthawi zambiri amagwera pamoto ndiponso mʼmadzi.+
15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa akudwala matenda akugwa ndipo akuvutika kwambiri. Nthawi zambiri amagwera pamoto ndiponso mʼmadzi.+