Aheberi 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro nʼzosatheka kusangalatsa Mulungu. Chifukwa aliyense wofuna kulambira Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi ndipo amapereka mphoto kwa anthu amene amamufunafuna ndi mtima wonse.+
6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro nʼzosatheka kusangalatsa Mulungu. Chifukwa aliyense wofuna kulambira Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi ndipo amapereka mphoto kwa anthu amene amamufunafuna ndi mtima wonse.+