2 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Davide anatonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kenako anagona naye ndipo patapita nthawi, anabereka mwana wamwamuna yemwe anamupatsa dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anamʼkonda mwana ameneyu,+ 1 Mbiri 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya, Sobabu, Natani+ ndi Solomo.+ Ana 4 amenewa mayi awo anali Bati-seba+ mwana wa Amiyeli.
24 Ndiyeno Davide anatonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kenako anagona naye ndipo patapita nthawi, anabereka mwana wamwamuna yemwe anamupatsa dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anamʼkonda mwana ameneyu,+
5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya, Sobabu, Natani+ ndi Solomo.+ Ana 4 amenewa mayi awo anali Bati-seba+ mwana wa Amiyeli.