Luka 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anayamba kuwauza kuti: “Lero lemba ili, limene mwangolimva kumeneli lakwaniritsidwa.”+