1 Mafumu 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kenako Solomo anamwalira* ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide bambo ake. Ndiyeno mwana wake Rehobowamu,+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
43 Kenako Solomo anamwalira* ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide bambo ake. Ndiyeno mwana wake Rehobowamu,+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.