Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komanso ngati diso lako limakuchimwitsa* ulikolowole nʼkulitaya kutali. Ndi bwino kuti ukapeze moyo uli ndi diso limodzi kusiyana nʼkuti uponyedwe mu Gehena* wamoto uli ndi maso onse awiri.+

  • Maliko 9:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Ngati diso lako limakuchimwitsa,* ulitaye.+ Ndi bwino kuti ukalowe mu Ufumu wa Mulungu uli ndi diso limodzi, kusiyana nʼkuti uponyedwe mu Gehena* uli ndi maso onse awiri,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena