32 Kodi mukamakonda anthu okhawo amene amakukondani, mudzapindula chiyani? Chifukwa ngakhale ochimwa amakonda anthu okhawo amene amawakonda.+ 33 Ngati mumachitira zabwino okhawo amene amakuchitirani zabwino, mudzapindula chiyani? Chifukwa ngakhale ochimwa amachita zomwezo.