Mateyu 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba timene amavala monga zodzitetezera,+ ndipo amatalikitsanso ulusi wopota wa mʼmphepete mwa zovala zawo.+
5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba timene amavala monga zodzitetezera,+ ndipo amatalikitsanso ulusi wopota wa mʼmphepete mwa zovala zawo.+