Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amene amakomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+Ndipo adzamʼbwezera* zimene anachitazo.+ Mateyu 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha mʼkapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira wanga, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pangʼono.”+
17 Amene amakomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+Ndipo adzamʼbwezera* zimene anachitazo.+
42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha mʼkapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira wanga, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pangʼono.”+