Mateyu 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mukamasala kudya,+ siyani kuonetsa nkhope yachisoni ngati mmene anthu achinyengo aja amachitira. Iwo sasamalira nkhope* zawo kuti anthu ena adziwe kuti akusala kudya.+ Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse. Mateyu 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba timene amavala monga zodzitetezera,+ ndipo amatalikitsanso ulusi wopota wa mʼmphepete mwa zovala zawo.+
16 Mukamasala kudya,+ siyani kuonetsa nkhope yachisoni ngati mmene anthu achinyengo aja amachitira. Iwo sasamalira nkhope* zawo kuti anthu ena adziwe kuti akusala kudya.+ Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.
5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba timene amavala monga zodzitetezera,+ ndipo amatalikitsanso ulusi wopota wa mʼmphepete mwa zovala zawo.+