Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+ Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu adziwe kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wamʼmwambamwamba, woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.+
3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+
18 Anthu adziwe kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wamʼmwambamwamba, woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.+