-
2 Mafumu 15:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Kenako Yotamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira, ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake. Ndiyeno mwana wake Ahazi anakhala mfumu mʼmalo mwake.
-