Miyambo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amene amalangiza wonyoza amachititsidwa manyazi,+Ndipo aliyense wodzudzula woipa adzavulazidwa. Mateyu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, mukamatuluka mʼnyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo muzisansa fumbi kumapazi anu.+
14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, mukamatuluka mʼnyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo muzisansa fumbi kumapazi anu.+