Luka 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Yesetsani mwamphamvu kuti mulowe pakhomo lalingʼono.+ Chifukwa ndithu ndikukuuzani, ambiri adzafunitsitsa kulowamo koma sadzatha.
24 “Yesetsani mwamphamvu kuti mulowe pakhomo lalingʼono.+ Chifukwa ndithu ndikukuuzani, ambiri adzafunitsitsa kulowamo koma sadzatha.