Mateyu 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nkhwangwa yaikidwa kale pamizu yamitengo. Choncho mtengo uliwonse wosabereka zipatso zabwino udulidwa nʼkuponyedwa pamoto.+ Luka 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mtengo wamkuyu mʼmunda wake wa mpesa, ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo, koma sanapezemo chilichonse.+ Luka 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ukadzabereka zipatso mʼtsogolo, zidzakhala bwino, koma ngati sudzabereka mudzaudule.’”+
10 Nkhwangwa yaikidwa kale pamizu yamitengo. Choncho mtengo uliwonse wosabereka zipatso zabwino udulidwa nʼkuponyedwa pamoto.+
6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mtengo wamkuyu mʼmunda wake wa mpesa, ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo, koma sanapezemo chilichonse.+