1 Akorinto 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ntchito ya aliyense idzadziwika kuti ndi yotani. Tsiku lina ntchitoyo idzadziwika mmene ilili, chifukwa moto ndi umene udzaonetsa zimenezo poyera.+ Motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.
13 ntchito ya aliyense idzadziwika kuti ndi yotani. Tsiku lina ntchitoyo idzadziwika mmene ilili, chifukwa moto ndi umene udzaonetsa zimenezo poyera.+ Motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.