2 Mafumu 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Komanso Farao Neko anaika Eliyakimu mwana wa Yosiya kukhala mfumu mʼmalo mwa Yosiya bambo ake, nʼkumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Atatero anatenga Yehoahazi nʼkupita naye ku Iguputo+ ndipo patapita nthawi anamwalira komweko.+
34 Komanso Farao Neko anaika Eliyakimu mwana wa Yosiya kukhala mfumu mʼmalo mwa Yosiya bambo ake, nʼkumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Atatero anatenga Yehoahazi nʼkupita naye ku Iguputo+ ndipo patapita nthawi anamwalira komweko.+