1 Mbiri 3:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya+ ndipo wa 4 anali Salumu. 16 Mwana wa Yehoyakimu+ anali Yekoniya. Yekoniya anabereka Zedekiya.
15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya+ ndipo wa 4 anali Salumu. 16 Mwana wa Yehoyakimu+ anali Yekoniya. Yekoniya anabereka Zedekiya.